Nyimbo imeneyi ikungotiunikira kuti kulibe kothawira kulikonse komwe tingathe kuyizemba infa.
Ngakhale tipite kuchipatala koma moyo wamunthu udzazima ndithu ndipo kulibe kuyipewa.
Pamene tikupita kutsogolo ndimoyo koma kokathera kwake ndi infa ndithu.
Palibe adzadumphe dzenje la infa.
2024